Salimo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu mwaona mavuto ndi masautso.Mumawayang’anabe kuti muchitepo kanthu.+Waumphawi,+ mwana wamasiye,* amadziikiza m’manja mwanu.Inu mwakhala mthandizi wake.+ Yeremiya 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo ine ndinali ngati mwana wa nkhosa wamphongo wokondedwa mwapadera, amene akupita kukaphedwa.+ Ine sindinadziwe kuti andikonzera ziwembu+ ndi kunena kuti: “Tiyeni tiwononge mtengowu pamodzi ndi zipatso zake. Tiyeni timuchotse m’dziko la anthu amoyo,+ kuti dzina lake lisakumbukikenso.”
14 Inu mwaona mavuto ndi masautso.Mumawayang’anabe kuti muchitepo kanthu.+Waumphawi,+ mwana wamasiye,* amadziikiza m’manja mwanu.Inu mwakhala mthandizi wake.+
19 Ndipo ine ndinali ngati mwana wa nkhosa wamphongo wokondedwa mwapadera, amene akupita kukaphedwa.+ Ine sindinadziwe kuti andikonzera ziwembu+ ndi kunena kuti: “Tiyeni tiwononge mtengowu pamodzi ndi zipatso zake. Tiyeni timuchotse m’dziko la anthu amoyo,+ kuti dzina lake lisakumbukikenso.”