Salimo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yehova adzakhala pampando wachifumu mpaka kalekale,+Adzakhazikitsa mpando wake wachifumu kuti aweruze.+ Salimo 90:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mapiri asanabadwe,+Kapena musanakhazikitse dziko lapansi+ ndi malo okhalapo anthu,*+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+ Salimo 102:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma inu Yehova, mudzakhalapobe kwamuyaya,+Dzina lanu* lidzakhalapobe ku mibadwomibadwo.+
7 Koma Yehova adzakhala pampando wachifumu mpaka kalekale,+Adzakhazikitsa mpando wake wachifumu kuti aweruze.+
2 Mapiri asanabadwe,+Kapena musanakhazikitse dziko lapansi+ ndi malo okhalapo anthu,*+Inu ndinu Mulungu kuyambira kalekale mpaka kalekale.+