Yesaya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kodi mumenyedwanso pati+ mmene mukupitiriza kupandukamu?+ Mutu wanu uli ndi zilonda zokhazokha, ndipo mtima wanu wafooka.+ Yeremiya 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndagwidwa ndi chisoni chosatha.+ Mtima wanga wadwala. Maliro 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa chifukwa chimenechi, mtima wathu wadwala.+ Chifukwa cha zinthu zimenezi, maso athu achita mdima.+
5 Kodi mumenyedwanso pati+ mmene mukupitiriza kupandukamu?+ Mutu wanu uli ndi zilonda zokhazokha, ndipo mtima wanu wafooka.+
17 Pa chifukwa chimenechi, mtima wathu wadwala.+ Chifukwa cha zinthu zimenezi, maso athu achita mdima.+