Yobu 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Khungu langa ndalisokera ziguduli*+ zoti livale,Ndipo ndaika nyanga yanga m’fumbi.+ Salimo 75:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mulungu akuti:* “Ndidzadula nyanga zonse za anthu oipa.”+Koma nyanga za munthu wolungama zidzakwezedwa.+
10 Mulungu akuti:* “Ndidzadula nyanga zonse za anthu oipa.”+Koma nyanga za munthu wolungama zidzakwezedwa.+