Yeremiya 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Musatulutse katundu aliyense kuchokera m’nyumba zanu pa tsiku la sabata ndipo musamagwire ntchito iliyonse.+ Tsiku la sabata muziliona kukhala lopatulika monga mmene ndinalamulira makolo anu.+
22 Musatulutse katundu aliyense kuchokera m’nyumba zanu pa tsiku la sabata ndipo musamagwire ntchito iliyonse.+ Tsiku la sabata muziliona kukhala lopatulika monga mmene ndinalamulira makolo anu.+