Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma ngati simudzamvera mawu a Yehova,+ moti n’kupandukiradi malamulo a Yehova,+ dzanja la Yehova lidzatsutsana ndi inu ndi abambo anu.+

  • 1 Samueli 15:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti kupanduka+ n’chimodzimodzi ndi tchimo la kuwombeza,+ ndipo kuchita zinthu modzikuza n’chimodzimodzi ndi kugwiritsa ntchito mphamvu zamatsenga ndiponso aterafi.+ Popeza iwe wakana mawu a Yehova,+ iyenso wakukana kuti usakhalenso mfumu.”+

  • Salimo 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mulungu adzawapeza ndi mlandu.+

      Adzagwa ndi ziwembu zawo zomwe.+

      Muwamwaze chifukwa cha kuchuluka kwa zolakwa zawo,+

      Chifukwa iwo akupandukirani.+

  • Yesaya 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma mukakana+ n’kupanduka, mudzawonongedwa ndi lupanga, chifukwa pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+

  • Yesaya 63:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma iwo anapanduka+ ndi kukhumudwitsa mzimu wake woyera.+ Chotero iye anasintha n’kukhala mdani+ wawo ndipo anachita nawo nkhondo.+

  • Ezekieli 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Posachedwapa, ndikukhuthulirani ukali wanga,+ ndipo mkwiyo wanga ndiuthetsera pa inu.+ Ndikuweruzani mogwirizana ndi njira zanu,+ ndipo ndikubwezerani chifukwa cha zonyansa zanu zonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena