Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+ Yeremiya 21:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndidzakuimbani mlandu+ mogwirizana ndi zipatso za ntchito zanu,’+ watero Yehova. ‘Ndidzayatsanso moto m’nkhalango za mzindawu,+ moti udzanyeketsa zinthu zonse zouzungulira.’”+
22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+
14 ndidzakuimbani mlandu+ mogwirizana ndi zipatso za ntchito zanu,’+ watero Yehova. ‘Ndidzayatsanso moto m’nkhalango za mzindawu,+ moti udzanyeketsa zinthu zonse zouzungulira.’”+