Deuteronomo 29:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mitundu yonse idzanena kuti, ‘N’chifukwa chiyani Yehova wachitira dzikoli zimenezi?+ N’chifukwa chiyani mkwiyo wake wayaka kwambiri chonchi?’ 1 Mafumu 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ineyo ndidzachotsa Aisiraeli padziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba imene ndaiyeretsa ndi dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Aisiraeli adzawapekera mwambi+ ndi kuwatonza pakati pa mitundu yonse ya anthu. Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]
24 Mitundu yonse idzanena kuti, ‘N’chifukwa chiyani Yehova wachitira dzikoli zimenezi?+ N’chifukwa chiyani mkwiyo wake wayaka kwambiri chonchi?’
7 ineyo ndidzachotsa Aisiraeli padziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba imene ndaiyeretsa ndi dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Aisiraeli adzawapekera mwambi+ ndi kuwatonza pakati pa mitundu yonse ya anthu.
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]