Yesaya 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, Manda* akulitsa malo ake ndipo atsegula kwambiri pakamwa pake kupitirira malire.+ Anthu olemekezeka a mumzindawo, khamu lake, phokoso lake ndi chikondwerero chake zidzatsikira m’mandamo.+
14 Choncho, Manda* akulitsa malo ake ndipo atsegula kwambiri pakamwa pake kupitirira malire.+ Anthu olemekezeka a mumzindawo, khamu lake, phokoso lake ndi chikondwerero chake zidzatsikira m’mandamo.+