1 Mafumu 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma sindidzachotsa ufumu wonse m’manja mwake. Ndidzamuika kukhala mtsogoleri masiku onse a moyo wake chifukwa cha Davide mtumiki wanga amene ndinamusankha,+ pakuti Davide anasunga malamulo anga ndi zigamulo zanga.
34 Koma sindidzachotsa ufumu wonse m’manja mwake. Ndidzamuika kukhala mtsogoleri masiku onse a moyo wake chifukwa cha Davide mtumiki wanga amene ndinamusankha,+ pakuti Davide anasunga malamulo anga ndi zigamulo zanga.