Salimo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tandipempha,+ ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kukhala cholowa chako,+Ndikupatsa dziko lonse lapansi kukhala lako.+ Danieli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako anamupatsa ulamuliro,+ ulemerero,+ ndi ufumu+ kuti anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana azimutumikira.+ Ulamuliro wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo sudzatha. Ufumu wake sudzawonongedwa.+ Luka 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho ndikuchita nanu pangano,+ mmene Atate wanga wachitira pangano la ufumu ndi ine,+
8 Tandipempha,+ ndipo ndikupatsa mitundu ya anthu kukhala cholowa chako,+Ndikupatsa dziko lonse lapansi kukhala lako.+
14 Kenako anamupatsa ulamuliro,+ ulemerero,+ ndi ufumu+ kuti anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana azimutumikira.+ Ulamuliro wake udzakhalapo mpaka kalekale ndipo sudzatha. Ufumu wake sudzawonongedwa.+