Salimo 119:119 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 119 Anthu onse oipa mwawachotsa padziko lapansi ngati zonyansa.*+N’chifukwa chake ine ndimakonda zikumbutso zanu.+ Miyambo 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Siliva akachotsedwa zotsalira pomuyenga, yense adzatuluka woyengeka bwino.+
119 Anthu onse oipa mwawachotsa padziko lapansi ngati zonyansa.*+N’chifukwa chake ine ndimakonda zikumbutso zanu.+