2 Mafumu 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero Ahazi anatumiza amithenga kwa Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri ndi uthenga wakuti: “Ndine mtumiki wanu+ ndi mwana wanu. Bwerani mudzandipulumutse+ m’manja mwa mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa mfumu ya Isiraeli, amene akundiukira.” 2 Mbiri 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa nthawi imeneyo, Mfumu Ahazi+ inatumiza uthenga kwa mafumu a Asuri+ kuti adzam’thandize.
7 Chotero Ahazi anatumiza amithenga kwa Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri ndi uthenga wakuti: “Ndine mtumiki wanu+ ndi mwana wanu. Bwerani mudzandipulumutse+ m’manja mwa mfumu ya Siriya ndi m’manja mwa mfumu ya Isiraeli, amene akundiukira.”