Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 19:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Usadane ndi m’bale wako mumtima mwako.+ Mnzako um’dzudzule ndithu+ kuti usasenze naye tchimo.

  • Ezekieli 33:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Koma mlondayo akaona lupanga likubwera, iye osaliza lipenga,+ anthu osamva chenjezo lililonse, lupangalo n’kufika ndi kupha anthu, anthuwo adzaphedwa chifukwa cha zolakwa zawo,+ koma magazi awo ndidzawafuna kuchokera m’manja mwa mlondayo.’+

  • Aheberi 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Muzimvera amene akutsogolera pakati panu+ ndipo muziwagonjera.+ Iwo amayang’anira miyoyo yanu monga anthu amene adzayankhe mlandu.+ Muziwamvera ndi kuwagonjera kuti agwire ntchito yawo mwachimwemwe, osati modandaula, pakuti akatero zingakhale zokuvulazani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena