2 Mafumu 24:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 komanso chifukwa cha magazi osalakwa+ amene iye anakhetsa, moti anadzaza Yerusalemu ndi magazi osalakwa, ndipo Yehova sanalole kukhululuka.+ Salimo 106:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho anali kukhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna ndi a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.+ Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+ Hoseya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kutembererana,+ kuchita zachinyengo,+ kuphana,+ kuba,+ ndi chigololo+ zafala m’dzikoli, ndipo kukhetsa magazi kukuchitika motsatizanatsatizana.+
4 komanso chifukwa cha magazi osalakwa+ amene iye anakhetsa, moti anadzaza Yerusalemu ndi magazi osalakwa, ndipo Yehova sanalole kukhululuka.+
38 Choncho anali kukhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna ndi a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.+
15 Mukatambasula manja anu,+ ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+ ine sindimvetsera.+ Manja anu adzaza magazi amene mwakhetsa.+
2 Kutembererana,+ kuchita zachinyengo,+ kuphana,+ kuba,+ ndi chigololo+ zafala m’dzikoli, ndipo kukhetsa magazi kukuchitika motsatizanatsatizana.+