Yobu 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Opulumuka ake adzaikidwa m’manda pa nthawi ya mliri wakupha,Ndipo akazi awo amasiye sadzalira.+ Salimo 78:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Ansembe ake anagwa ndi lupanga,+Ndipo akazi awo amasiye sanalire.+