Ezekieli 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pa chifukwa chimenechi, ndikuperekani kwa anthu a Kum’mawa kuti mukhale chuma chawo.+ Iwo adzamanga misasa yokhala ndi mipanda ndiponso mahema awo m’dziko lanu. Adzadya zokolola zanu ndi kumwa mkaka wanu.+
4 Pa chifukwa chimenechi, ndikuperekani kwa anthu a Kum’mawa kuti mukhale chuma chawo.+ Iwo adzamanga misasa yokhala ndi mipanda ndiponso mahema awo m’dziko lanu. Adzadya zokolola zanu ndi kumwa mkaka wanu.+