Ezekieli 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mudzakhala ngati nkhuni pamoto.+ Magazi anu adzayenderera m’dzikolo. Inu simudzakumbukiridwanso, pakuti ine Yehova ndanena.’”+
32 Mudzakhala ngati nkhuni pamoto.+ Magazi anu adzayenderera m’dzikolo. Inu simudzakumbukiridwanso, pakuti ine Yehova ndanena.’”+