Ezekieli 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Udzakhala chitonzo+ ndi chinthu chochilankhulira mawu onyoza.+ Udzakhalanso chenjezo+ ndi choopsezera mitundu yokuzungulira ndikadzakuweruza mokwiya komanso mwaukali, ndiponso ndikadzakulanga mokwiya.+ Ineyo Yehova ndi amene ndanena zimenezi. Nahumu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+
15 Udzakhala chitonzo+ ndi chinthu chochilankhulira mawu onyoza.+ Udzakhalanso chenjezo+ ndi choopsezera mitundu yokuzungulira ndikadzakuweruza mokwiya komanso mwaukali, ndiponso ndikadzakulanga mokwiya.+ Ineyo Yehova ndi amene ndanena zimenezi.
2 Yehova ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha+ ndipo amabwezera adani ake.+ Yehova amabwezera adani ake ndipo ndi waukali.+ Yehova amabwezera adani ake+ ndipo saiwala zoipa zimene iwo anachita.+