Deuteronomo 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+ Salimo 81:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikanagonjetsa adani awo mosavuta,+Ndipo ndikanalanga adani awo ndi dzanja langa.+ Salimo 97:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patsogolo pake pakuyaka moto,+Ndipo ukupsereza adani ake onse omuzungulira.+
41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+