Ezekieli 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Onse okudziwa pakati pa mitundu ya anthu adzakuyang’anitsitsa modabwa.+ Zoopsa zodzidzimutsa zidzakugwera ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.”’”+
19 Onse okudziwa pakati pa mitundu ya anthu adzakuyang’anitsitsa modabwa.+ Zoopsa zodzidzimutsa zidzakugwera ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.”’”+