Ezekieli 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Ndidzakugwetsera zoopsa modzidzimutsa+ ndipo sudzakhalaponso. Anthu adzakufunafuna+ koma sudzapezeka mpaka kalekale,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.” Ezekieli 27:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Amalonda ochokera pakati pa mitundu ina ya anthu adzakuimbira miluzu.+ Zoopsa zodzidzimutsa zidzakugwera ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.’”’”+
21 “‘Ndidzakugwetsera zoopsa modzidzimutsa+ ndipo sudzakhalaponso. Anthu adzakufunafuna+ koma sudzapezeka mpaka kalekale,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
36 Amalonda ochokera pakati pa mitundu ina ya anthu adzakuimbira miluzu.+ Zoopsa zodzidzimutsa zidzakugwera ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.’”’”+