Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+ Ezekieli 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzakusandutsa malo osalala apathanthwe lopanda kanthu.+ Udzakhala malo oyanikapo makoka.+ Iwe sudzamangidwanso, pakuti ine Yehova ndanena,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+
10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+
14 Ndidzakusandutsa malo osalala apathanthwe lopanda kanthu.+ Udzakhala malo oyanikapo makoka.+ Iwe sudzamangidwanso, pakuti ine Yehova ndanena,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.+