Ekisodo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+ Ezekieli 39:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu onse a m’dzikolo adzagwira ntchito yofotsera mitembo. Iwo adzatchuka chifukwa cha ntchito imeneyi pa tsiku limene ine ndidzalemekezeke,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
16 Koma ndakusiya ndi moyo+ kuti ndikusonyeze mphamvu zanga, ndi kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+
13 Anthu onse a m’dzikolo adzagwira ntchito yofotsera mitembo. Iwo adzatchuka chifukwa cha ntchito imeneyi pa tsiku limene ine ndidzalemekezeke,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.