Yesaya 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova adzakantha Iguputo.+ Adzamukantha n’kumuchiza,+ ndipo iwo adzabwerera kwa Yehova.+ Iye adzamva kuchonderera kwawo ndipo adzawachiritsa.+ Yeremiya 46:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Ndidzapereka anthu a ku Iguputo m’manja mwa anthu amene akufuna moyo wawo, m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo+ ndi m’manja mwa atumiki ake. Kenako anthu adzakhalanso m’dzikolo monga mmene zinalili kale,’+ watero Yehova.
22 Yehova adzakantha Iguputo.+ Adzamukantha n’kumuchiza,+ ndipo iwo adzabwerera kwa Yehova.+ Iye adzamva kuchonderera kwawo ndipo adzawachiritsa.+
26 “‘Ndidzapereka anthu a ku Iguputo m’manja mwa anthu amene akufuna moyo wawo, m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo+ ndi m’manja mwa atumiki ake. Kenako anthu adzakhalanso m’dzikolo monga mmene zinalili kale,’+ watero Yehova.