Salimo 79:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+ Yesaya 64:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu Yehova musatikwiyire kwambiri,+ ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.+ Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndife anthu anu.+
8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+
9 Inu Yehova musatikwiyire kwambiri,+ ndipo musakumbukire zolakwa zathu kwamuyaya.+ Chonde, kumbukirani kuti tonsefe ndife anthu anu.+