Salimo 110:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+ Yesaya 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’tsiku limenelo Yehova adzakumbukira makamu akumwamba ndi mafumu a padziko lapansi.+ Zekariya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova adzapita kukamenyana ndi anthu a mitundu inawo+ ngati mmene anachitira pomenyana ndi adani ake m’mbuyomu.+
6 Adzapereka chiweruzo pakati pa anthu a mitundu ina.+Adzachititsa mitembo ya anthu kupezeka paliponse.+Adzaphwanyaphwanya mtsogoleri wa dziko la anthu ambiri.+
3 “Yehova adzapita kukamenyana ndi anthu a mitundu inawo+ ngati mmene anachitira pomenyana ndi adani ake m’mbuyomu.+