Ekisodo 15:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu adzamva+ ndipo adzatekeseka.+Okhala ku Filisitiya adzamva zopweteka ngati za pobereka.+