1 Mbiri 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ana a Yafeti anali Gomeri, Magogi,+ Madai,+ Yavani,+ Tubala, Meseke,+ ndi Tirasi.+ Ezekieli 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Iwe mwana wa munthu, losera zoipa zimene zidzachitikire Gogi.+ Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndithana nawe iwe Gogi, mtsogoleri wamkulu wa Meseke+ ndi Tubala.+
39 “Iwe mwana wa munthu, losera zoipa zimene zidzachitikire Gogi.+ Unene kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndithana nawe iwe Gogi, mtsogoleri wamkulu wa Meseke+ ndi Tubala.+