Ezekieli 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tayani zolakwa zanu zonse zimene munachita+ ndipo muyesetse kukhala ndi mtima watsopano+ ndiponso mzimu watsopano.+ Kodi muferenji+ inu a nyumba ya Isiraeli?’ 2 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+
31 Tayani zolakwa zanu zonse zimene munachita+ ndipo muyesetse kukhala ndi mtima watsopano+ ndiponso mzimu watsopano.+ Kodi muferenji+ inu a nyumba ya Isiraeli?’
9 Yehova sakuchedwa kukwaniritsa lonjezo lake,+ ngati mmene anthu ena amaonera kuti akuchedwa, koma akuleza nanu mtima, pakuti safuna kuti wina aliyense adzawonongedwe, koma amafuna kuti anthu onse alape.+