Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 3:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu wolungama akasiya chilungamo chake+ n’kumachita zinthu zopanda chilungamo, ine n’kumuikira chopunthwitsa pamaso pake,+ iyeyo adzafa chifukwa chakuti sunamuchenjeze. Adzafa chifukwa cha tchimo lake+ ndipo zinthu zolungama zimene anachita sizidzakumbukiridwa,+ koma magazi ake ndidzawafuna kwa iweyo.+

  • Ezekieli 18:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “‘Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo,+ akamachita zopanda chilungamo+ n’kumakhalabe ndi moyo, zinthu zolungama zonse zimene anachita sizidzakumbukiridwa.+ Iye adzafa chifukwa chochita zinthu mosakhulupirika ndiponso chifukwa cha machimo ake amene anachita.+

  • 2 Petulo 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndithudi, ngati anapulumuka ku zoipitsa za dzikoli+ mwa kumudziwa molondola Ambuye ndi Mpulumutsi Yesu Khristu, koma alowereranso m’zinthu zomwe zija ndi kugonjetsedwa nazo,+ potsirizira pake makhalidwe awo amakhala oipa kwambiri kuposa poyamba.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena