Yeremiya 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndiyeno anthuwo n’kumachita zoipa pamaso panga mwa kusamvera mawu anga,+ pamenepo ndidzasintha maganizo anga pa zabwino zimene ndinali kufuna kudzawachitira pofuna kuwapindulitsa.’ Ezekieli 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+
10 ndiyeno anthuwo n’kumachita zoipa pamaso panga mwa kusamvera mawu anga,+ pamenepo ndidzasintha maganizo anga pa zabwino zimene ndinali kufuna kudzawachitira pofuna kuwapindulitsa.’
4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+