Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno khoma la mzindawo linabooledwa,+ ndipo amuna onse ankhondo anathawa usiku kudzera pachipata chimene chinali pakati pa makoma awiri, pafupi ndi munda wa mfumu.+ Akasidi+ anali atazungulira mzinda wonsewo, ndipo mfumuyo inayamba kuthawa+ kulowera cha ku Araba.+

  • 2 Mbiri 36:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.

  • Yeremiya 39:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’chaka cha 11 cha ulamuliro wa Zedekiya, m’mwezi wachinayi, pa tsiku la 9, anaboola mpanda wa mzindawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena