Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 39:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno ena mwa anthuwo, anthu onyozeka amene analibe kalikonse, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anawasiya m’dziko la Yuda,+ ndipo pa tsiku limenelo anawapatsa minda ya mpesa ndi ntchito zokakamiza kuti azigwira.+

  • Ezekieli 36:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tsopano inu mapiri a ku Isiraeli,+ tamverani mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, walankhula ndi mapiri, zitunda, mitsinje, zigwa ndi malo owonongedwa amene ndi mabwinja.+ Walankhulanso ndi mizinda yopanda anthu imene anthu otsala a mitundu ina anaitenga kukhala yawo. Anthuwo anakhala moizungulira ndipo amainyoza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena