Salimo 79:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu oyandikana nafe akutitonza,+Anthu otizungulira akutinyoza ndi kutiseka.+ Ezekieli 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Iwo sadzabedwanso ndi anthu a mitundu ina.+ Chilombo chakutchire sichidzawadyanso. Adzakhala mwabata popanda wowaopsa.+
28 Iwo sadzabedwanso ndi anthu a mitundu ina.+ Chilombo chakutchire sichidzawadyanso. Adzakhala mwabata popanda wowaopsa.+