Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.] Yeremiya 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu.+ Mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, malo opanda wokhalamo.+ Yeremiya 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+ Yeremiya 32:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Anthu adzagula minda m’dziko lino,+ dziko limene anthu inu mudzanena kuti: “Dziko ili ndi bwinja,+ lopanda munthu wokhalamo kapena nyama yoweta. Linaperekedwa m’manja mwa Akasidi.”’+
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]
11 Yerusalemu ndidzamusandutsa milu ya miyala+ ndiponso malo obisalamo mimbulu.+ Mizinda ya Yuda ndidzaisandutsa mabwinja, malo opanda wokhalamo.+
11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+
43 Anthu adzagula minda m’dziko lino,+ dziko limene anthu inu mudzanena kuti: “Dziko ili ndi bwinja,+ lopanda munthu wokhalamo kapena nyama yoweta. Linaperekedwa m’manja mwa Akasidi.”’+