Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yesuruni*+ atayamba kunenepa, anayamba kupanduka.+

      Iwe wanenepa, wakulupala, wakhuta mopitirira muyezo.+

      Pamenepo iye anasiya Mulungu amene anam’panga,+

      Ndi kunyoza Thanthwe+ la chipulumutso chake.

  • Yesaya 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Chotero Ambuye woona, Yehova wa makamu azidzatumizira anthu ake* onenepa nthenda yowondetsa,+ ndipo pansi pa ulemerero wake pazidzangoyaka, ngati kuyaka kwa moto.+

  • Amosi 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Tamverani mawu awa, inu ng’ombe zazikazi za ku Basana,+ zokhala m’phiri la Samariya,+ inu amene mukuchitira zachinyengo anthu onyozeka,+ amene mukuphwanya anthu osauka ndipo mukuuza ambuye anu kuti, ‘Tipatseni chakumwa kuti timwe!’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena