Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Zekariya 11:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Amene anazigula anazipha+ koma sanaimbidwe mlandu.+ Amene akuzigulitsa+ akunena kuti: “Yehova atamandike pamene ine ndikupeza chuma.”+ Abusa ake sazichitira chifundo ngakhale pang’ono.’+

  • Zekariya 11:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti ndilola kuti m’dzikoli mukhale m’busa wina.+ M’busa ameneyu sadzasamala nkhosa zimene zikuwonongeka.+ Nkhosa yaing’ono sadzaifunafuna, ndipo yothyoka sadzaichiritsa.+ Nkhosa yotha kuima yokha sadzaipatsa chakudya, ndipo adzadya nyama ya nkhosa yonenepa.+ Iye adzakupula ziboda za nkhosazo.+

  • Luka 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma mtsogoleri wa sunagoge ataona izi, anakwiya chifukwa Yesu anachiritsa munthu pa sabata.+ Choncho anayamba kuuza khamu la anthu kuti: “Pali masiku 6 oyenera kugwira ntchito. Muzibwera masiku amenewo kudzachiritsidwa, osati tsiku la sabata.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena