Salimo 85:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova nayenso adzapereka zinthu zabwino,+Ndipo dziko lathu lidzapereka zipatso zake.+ Ezekieli 36:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzachulukitsa zipatso za mtengo ndi zokolola zakumunda kuti musadzanyozekenso chifukwa cha njala pakati pa mitundu ina ya anthu.+
30 Ndidzachulukitsa zipatso za mtengo ndi zokolola zakumunda kuti musadzanyozekenso chifukwa cha njala pakati pa mitundu ina ya anthu.+