Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 34:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mtengo wam’munda udzabereka zipatso.+ Nthaka idzatulutsa zokolola zake.+ Iwo adzakhala m’dziko lawo mwabata.+ Ndikadzathyola goli lawo+ ndi kuwapulumutsa m’dzanja la amene anali kuwagwiritsa ntchito monga akapolo,+ adzadziwa kuti ine ndine Yehova.

  • Ezekieli 36:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma inu mapiri a Isiraeli, mudzatulutsa nthambi ndi kubalira zipatso anthu anga Aisiraeli,+ chifukwa chakuti atsala pang’ono kulowa m’dziko lino.+

  • Ezekieli 36:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Anthu adzanena kuti: “Dziko ilo limene linali bwinja tsopano lakhala ngati munda wa Edeni.+ Mizinda imene inawonongedwa ija, imene inali mabwinja ndiponso imene nyumba zake zinagwetsedwa, tsopano ili ndi mipanda yolimba kwambiri ndipo mukukhala anthu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena