Salimo 94:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi amene anakupatsani makutu, sangamve?+Kapena amene anapanga maso, sangaone?+