-
Salimo 98:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mitsinje iwombe m’manja,
Mapiri onse afuule pamodzi mokondwera pamaso pa Yehova.+
-
Yesaya 44:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 “Fuulani mokondwa kumwamba inu,+ pakuti Yehova wachitapo kanthu.+ Fuulani mosangalala,+ inu malo otsika kwambiri a dziko lapansi.+ Mapiri+ inu ndiponso iwe nkhalango ndi inu mitengo yonse ili mmenemo, kondwani ndi kufuula ndi chisangalalo. Pakuti Yehova wawombola Yakobo ndipo wasonyeza kukongola kwake pa Isiraeli.”+
-
-
-