Salimo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuti apulumutse moyo wawo ku imfa,+Ndi kuwasunga ndi moyo pa nthawi ya njala.+ Ezekieli 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘“Ndidzawapatsa munda wotchuka+ ndipo sadzafa ndi njala m’dzikomo.+ Mitundu ina ya anthu sidzawanyozanso.+
29 “‘“Ndidzawapatsa munda wotchuka+ ndipo sadzafa ndi njala m’dzikomo.+ Mitundu ina ya anthu sidzawanyozanso.+