Ezekieli 36:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ‘Ndidzathetsa nkhani zonyoza zimene anthu a mitundu ina amakunenerani.+ Mitundu ya anthu sidzakunyozaninso+ ndipo simudzakhumudwitsanso mitundu ya anthu okhala mwa inu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
15 ‘Ndidzathetsa nkhani zonyoza zimene anthu a mitundu ina amakunenerani.+ Mitundu ya anthu sidzakunyozaninso+ ndipo simudzakhumudwitsanso mitundu ya anthu okhala mwa inu,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”