Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+

      Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+

      Kodi ananenapo kanthu koma osachita,

      Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+

  • Ezekieli 22:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kodi mtima wako udzapitiriza kupirira,+ kapena kodi manja ako adzakhala ndi mphamvu m’masiku amene ndidzakulange?+ Ine Yehova ndanena ndipo ndidzachitapo kanthu.+

  • Ezekieli 28:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Adzakhala m’dzikolo popanda chowaopseza,+ adzamanga nyumba+ ndi kulima minda ya mpesa.+ Iwo adzakhala mwabata+ ndikadzapereka chiweruzo kwa onse owazungulira amene akuwatonza.+ Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo.”’”

  • Ezekieli 37:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 ‘Ndidzaika mzimu wanga mwa inu ndipo mudzakhala amoyo.+ Ndidzakukhazikani m’dziko lanu ndipo mudzadziwa kuti ine Yehova ndinanena zimenezi ndipo ndazichita,’ watero Yehova.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena