Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 102:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iye adzamvetsera pemphero la anthu amene alandidwa chilichonse,+

      Ndipo sadzapeputsa pemphero lawo.+

  • Yesaya 55:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu inu funafunani Yehova pamene iye akupezekabe.+ Muitaneni akadali pafupi.+

  • Yeremiya 29:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 ‘Mudzaitanira pa ine komanso mudzabwera ndi kupemphera kwa ine ndipo ine ndidzakumvetserani.’+

  • Yeremiya 50:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iwo adzafunsira njira yopita ku Ziyoni nkhope zawo zitayang’ana kumeneko.+ Iwo adzanena kuti, ‘Bwerani, tiyeni tidziphatike kwa Yehova mwa kuchita pangano lokhalapo mpaka kalekale limene silidzaiwalika.’+

  • Zekariya 13:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Ine ndidzatenga gawo lachitatulo n’kuliika pamoto+ kuti liyengeke. Ndidzawayenga ngati mmene amayengera siliva+ ndi kuwayeza ngati mmene amayezera golide.+ Gawo limeneli la anthu lidzaitana dzina langa, ndipo ine ndidzawayankha.+ Ndidzanena kuti, ‘Awa ndi anthu anga,’+ ndipo iwo adzanena kuti, ‘Yehova ndi Mulungu wathu.’”+

  • Mateyu 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Pemphanibe,+ ndipo adzakupatsani. Pitirizani kufunafuna, ndipo mudzapeza. Gogodanibe,+ ndipo adzakutsegulirani.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena