Ezekieli 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzimu unandinyamula+ moti ndinapita ndili wachisoni ndi wokwiya kwambiri mumtima mwanga, ndipo dzanja la Yehova linandigwira mwamphamvu.+ Chivumbulutso 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho, mu mphamvu ya mzimu, ananditengera kuphiri lalikulu ndi lalitali,+ ndipo anandionetsa mzinda woyera,+ Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+
14 Mzimu unandinyamula+ moti ndinapita ndili wachisoni ndi wokwiya kwambiri mumtima mwanga, ndipo dzanja la Yehova linandigwira mwamphamvu.+
10 Choncho, mu mphamvu ya mzimu, ananditengera kuphiri lalikulu ndi lalitali,+ ndipo anandionetsa mzinda woyera,+ Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+