Ezekieli 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ndinalosera monga mmene anandiuzira ndipo mpweya unalowa mwa anthuwo. Iwo anakhala ndi moyo ndipo anaimirira.+ Anali khamu lalikulu la gulu lankhondo.
10 Pamenepo ndinalosera monga mmene anandiuzira ndipo mpweya unalowa mwa anthuwo. Iwo anakhala ndi moyo ndipo anaimirira.+ Anali khamu lalikulu la gulu lankhondo.