Chivumbulutso 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya.+ Atatero, kunamveka mawu ofuula+ kuchokera m’malo opatulika, kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!”
17 Ndiyeno mngelo wa 7 anakhuthulira mbale yake pampweya.+ Atatero, kunamveka mawu ofuula+ kuchokera m’malo opatulika, kuchokera kumpando wachifumu, akuti: “Zachitika!”