Chivumbulutso 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma ena onse anaphedwa ndi lupanga lalitali la wokwera pahatchi,+ limene linatuluka m’kamwa mwake lija.+ Ndipo mbalame+ zonse zinakhuta+ minofu yawo.+
21 Koma ena onse anaphedwa ndi lupanga lalitali la wokwera pahatchi,+ limene linatuluka m’kamwa mwake lija.+ Ndipo mbalame+ zonse zinakhuta+ minofu yawo.+